ecz cinyanja 2016 paper 1
Funso lirilonse liyamba ndi ciganizo comwe ciri ndi liu kapena dera lina losowa m’malo amene aonetsedwa. Munsi mwake mudzapezamo mau kapena madera a ziganizo anai. Liu limodzi mwa mau anai ndilo litsiriza bwino ciganizo conse.